-
Salimo 35:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Njira yawo ikhale yamdima ndi yoterera
Pamene mngelo wa Yehova akuwathamangitsa.
7 Popanda chifukwa, iwo atchera ukonde kuti andikole.
Akumba dzenje kuti ndigweremo ngakhale kuti sindinalakwe.
-