-
Salimo 37:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Koma oipa onse adzatheratu,+
Adani a Yehova adzasowa mofulumira ngati malo okongola odyetsera ziweto amene msipu wake wobiriwira suchedwa kufota.
Iwo adzatha mofulumira ngati utsi.
-