Salimo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adzatsogolera ofatsa kuti azichita zinthu zoyenera,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuti aziyenda mʼnjira yake.+ Salimo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 37:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yehova akasangalala ndi njira za munthu+Amamusonyeza zoyenera kuchita pa moyo wake.+ Salimo 143:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Miyambo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
9 Adzatsogolera ofatsa kuti azichita zinthu zoyenera,+Ndipo adzaphunzitsa ofatsa kuti aziyenda mʼnjira yake.+