Salimo 42:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mofanana ndi munthu amene akulakalaka madzi, ndikulakalaka* Mulungu, Mulungu wamoyo.+ Ndidzapita liti kukaonekera pamaso pa Mulungu?*+ Salimo 84:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+
2 Mofanana ndi munthu amene akulakalaka madzi, ndikulakalaka* Mulungu, Mulungu wamoyo.+ Ndidzapita liti kukaonekera pamaso pa Mulungu?*+
9 Usiku ndimakulakalakani ndi mtima wanga wonse,Inde, ndimakufunafunani ndi mtima wonse.+Chifukwa mukaweruza dziko lapansi,Anthu okhala mʼdzikoli amaphunzira zokhudza chilungamo.+