-
Yesaya 31:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Msuri adzaphedwa ndi lupanga, koma osati la munthu.
Lupanga lidzamudya, koma osati la munthu.+
Iye adzathawa chifukwa cha lupangalo
Ndipo anyamata ake adzagwiritsidwa ntchito yaukapolo.
-
-
Yesaya 37:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Ndiyeno mngelo wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri nʼkukapha asilikali 185,000. Anthu podzuka mʼmawa, anangoona kuti onse ndi mitembo yokhayokha.+
-