Salimo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mawu a Yehova akumveka pamwamba pa madzi,Mawu a Mulungu waulemerero akugunda ngati bingu.+ Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+
3 Mawu a Yehova akumveka pamwamba pa madzi,Mawu a Mulungu waulemerero akugunda ngati bingu.+ Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+