Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Numeri 14:19, 20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chonde, khululukani zolakwa za anthuwa mogwirizana ndi chikondi chanu chokhulupirika chomwe ndi chachikulu, ngati mmene mwakhala mukuwakhululukira kuchokera ku Iguputo mpaka pano.”+

      20 Ndiyeno Yehova anati: “Chabwino, ndawakhululukira mogwirizana ndi zimene wanena.+

  • Yeremiya 30:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa ine ndili ndi iwe kuti ndikupulumutse,” akutero Yehova.

      “Ndidzawononga anthu a mitundu yonse yakumene ndinakubalalitsirani.+

      Koma iweyo sindidzakuwononga.+

      Ndidzakulanga* pamlingo woyenera,

      Ndipo sindidzakusiya osakupatsa chilango.”+

  • Maliro 3:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chifukwa cha chikondi chokhulupirika cha Yehova, ife sitinatheretu,+

      Ndipo chifundo chake sichitha.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani