-
Yeremiya 7:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Mitembo ya anthu awa idzakhala chakudya cha mbalame zouluka mumlengalenga ndi cha zilombo ndipo sipadzakhala woziopseza.+
-
-
Yeremiya 34:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndidzawapereka mʼmanja mwa adani awo ndi mʼmanja mwa onse amene akufuna moyo wawo. Mitembo yawo idzakhala chakudya cha mbalame zouluka mumlengalenga ndi zilombo zakutchire.+
-