-
Deuteronomo 28:37Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
37 Anthu adzachita mantha akadzaona zimene zakuchitikirani ndipo mudzatonzedwa ndi kunyozedwa pakati pa mitundu yonse ya anthu kumene Yehova akukuthamangitsirani.+
-
-
Ezekieli 36:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho inu mapiri a ku Isiraeli, imvani mawu a Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza mapiri ndi zitunda, mitsinje ndi zigwa, mabwinja a malo amene anawonongedwa+ komanso mizinda yopanda anthu imene anthu a mitundu ina amene anapulumuka anaitenga kuti ikhale yawo. Anthuwo ankakhala moizungulira ndipo ankainyoza.+
-