-
Salimo 145:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Anthu adzatamanda ntchito zanu ku mibadwomibadwo.
Adzanena za ntchito zanu zamphamvu.+
-
-
Yesaya 43:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiponso kuti anthu amene ndinawapanga kuti akhale anga,
Alengeze za ulemerero wanga.+
-