-
Oweruza 8:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Pa nthawiyi nʼkuti Zeba ndi Zalimuna ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kumʼmawa+ chifukwa asilikali 120,000 anali ataphedwa.
-
-
Oweruza 8:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Zeba ndi Zalimuna atayamba kuthawa, iye anawathamangitsa mpaka kuwagwira. Mafumu a Midiyaniwa atagwidwa, gulu lawo lonse linachita mantha.
-