-
Salimo 130:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Isiraeli apitirize kuyembekezera Yehova,
Chifukwa Yehova amasonyeza chikondi chokhulupirika,+
Ndipo ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu.
-