Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • Misonkhano
  • Salimo 27:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndilangizeni, inu Yehova, kuti ndiyende mʼnjira yanu.+

      Nditsogolereni mʼnjira yoyenera kuti nditetezeke kwa adani anga.

  • Salimo 119:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiphunzitseni inu Yehova,+ kuti ndizichita zinthu mogwirizana ndi malangizo anu,

      Ndipo ndidzawatsatira kwa moyo wanga wonse.+

  • Salimo 143:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Mʼmawa ndichititseni kumva za chikondi chanu chokhulupirika,

      Chifukwa ndimadalira inu.

      Ndidziwitseni njira imene ndikuyenera kuyendamo,+

      Chifukwa ndimadalira inu kuti muzinditsogolera.*

  • Yesaya 54:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana ako onse azidzaphunzitsidwa ndi Yehova,+

      Ndipo mtendere wa ana ako udzakhala wochuluka.+

Mabuku a Chinenero Chamanja cha ku Malawi (1993-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chinenero Chamanja cha ku Malawi
  • tumizirani
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • zachinsinsi
  • JW.ORG
  • Lowani
tumizirani