Salimo 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 31:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mudzawabisa mʼmalo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa kwa anthu amene awakonzera chiwembu.Mudzawabisa mʼmalo anu otetezekaKuti anthu amene akuwanyoza asawapeze.*+ Salimo 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
20 Mudzawabisa mʼmalo otetezeka pafupi ndi inu,+Kuwachotsa kwa anthu amene awakonzera chiwembu.Mudzawabisa mʼmalo anu otetezekaKuti anthu amene akuwanyoza asawapeze.*+