-
Salimo 121:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Taonani! Amene akuyangʼanira Isiraeli,+
Sadzawodzera kapena kugona.
-
-
Yesaya 60:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Taona! Mdima udzaphimba dziko lapansi,
Ndipo mdima wandiweyani udzaphimba mitundu ya anthu.
Koma kuwala kwa Yehova kudzafika pa iwe,
Ndipo ulemerero wake udzaonekera pa iwe.
-