Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+ Yesaya 44:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi pali aliyense wopusa amene angafike popanga mulungu kapena fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,*Lomwe ndi lopanda phindu?+
7 Onse amene akutumikira chifaniziro chilichonse achite manyazi,+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yawo yopanda pake.+ Muweramireni,* inu milungu yonse.+
10 Kodi pali aliyense wopusa amene angafike popanga mulungu kapena fano lopangidwa ndi chitsulo chosungunula,*Lomwe ndi lopanda phindu?+