-
Malaki 4:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 “Taonani! Tsiku loyaka ngati ngʼanjo likubwera,+ ndipo anthu onse odzikuza ndi onse ochita zoipa adzakhala ngati mapesi. Pa tsikulo iwo adzawonongedwa moti sipadzatsala mizu kapena nthambi zawo,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-