Oweruza 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri anasungunuka* pamaso pa Yehova,+Ngakhalenso Sinai anasungunuka pamaso pa Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.+ Nahumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri akuluakulu amagwedezeka chifukwa cha iye.Ndipo mapiri angʼonoangʼono amasungunuka.+ Dziko lapansi lidzanjenjemera chifukwa cha nkhope yakePamodzi ndi nthaka komanso zinthu zonse zokhala mʼdzikomo.+ Habakuku 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
5 Mapiri anasungunuka* pamaso pa Yehova,+Ngakhalenso Sinai anasungunuka pamaso pa Yehova,+ Mulungu wa Isiraeli.+
5 Mapiri akuluakulu amagwedezeka chifukwa cha iye.Ndipo mapiri angʼonoangʼono amasungunuka.+ Dziko lapansi lidzanjenjemera chifukwa cha nkhope yakePamodzi ndi nthaka komanso zinthu zonse zokhala mʼdzikomo.+