-
Mika 7:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndidzapirira mkwiyo wa Yehova,
Chifukwa ndamuchimwira.+
Ndidzaupirira mpaka ataweruza mlandu wanga nʼkundichitira chilungamo.
Iye adzandipititsa pamalo owala,
Ndipo ndidzaona chilungamo chake.
-