-
Salimo 95:6, 7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Bwerani, tiyeni timulambire komanso kumugwadira.
Tiyeni tigwade pamaso pa Yehova amene anatipanga.+
7 Chifukwa iye ndi Mulungu wathu
Ndipo ife ndi anthu amene iye akuweta,
Lero anthu inu mukamvera mawu ake,+
-
Ezekieli 34:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 ‘Koma inu nkhosa zanga,+ nkhosa zimene ndikuzisamalira, ndinu anthu basi ndipo ine ndine Mulungu wanu,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-
-
-