Salimo 51:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chimene chimabwera chifukwa cha chipulumutso chanu.+Ndipatseni mtima wofunitsitsa kukumverani.* Yesaya 40:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
12 Bwezeretsani mwa ine chisangalalo chimene chimabwera chifukwa cha chipulumutso chanu.+Ndipatseni mtima wofunitsitsa kukumverani.*