-
Salimo 145:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ufumu wanu ndi ufumu wamuyaya,
Ndipo ulamuliro wanu udzakhalapo ku mibadwo yonse.+
-
-
Danieli 4:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Inuyo adzakuthamangitsani pakati pa anthu ndipo muzidzakhala ndi nyama zakutchire. Muzidzadya udzu ngati ngʼombe ndipo muzidzanyowa ndi mame akumwamba.+ Ndiyeno padzadutsa+ nthawi zokwana 7+ mpaka mutadziwa kuti Mulungu Wamʼmwambamwamba ndi Wolamulira wa maufumu a anthu ndiponso kuti amapereka ulamuliro kwa aliyense amene akufuna kumupatsa.+
-