-
Numeri 16:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Nthawi yomweyo anthuwo anachoka kumbali zonse za matenti a Kora, Datani ndi Abiramu. Zitatero, Datani ndi Abiramu anatuluka nʼkuima pamakomo a matenti awo, limodzi ndi akazi awo, ana awo aamuna komanso ana awo angʼonoangʼono.
-