- 
	                        
            
            Yoswa 17:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        12 Koma ana a Manase analephera kulanda mizindayi, moti Akanani anakakamira kukhalabe mʼderali.+ 
 
- 
                                        
- 
	                        
            
            Oweruza 1:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        21 Anthu a fuko la Benjamini sanathamangitse Ayebusi a ku Yerusalemu, moti Ayebusiwo akukhalabe ndi anthu a fuko la Benjamini ku Yerusalemu mpaka lero.+ 
 
-