Deuteronomo 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angathamangitse bwanji anthu 10,000?+ Nʼzosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka. Oweruza 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka* kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.* Aisiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.
30 Kodi munthu mmodzi angathamangitse bwanji anthu 1,000,Kapena anthu awiri angathamangitse bwanji anthu 10,000?+ Nʼzosatheka, pokhapokha Thanthwe lawo litawagulitsa,+Komanso ngati Yehova atawapereka.
8 Zitatero Yehova anakwiyira kwambiri Aisiraeli, moti anawapereka* kwa Kusani-risataimu, mfumu ya Mesopotamiya.* Aisiraeli anatumikira Kusani-risataimu zaka 8.