Oweruza 10:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma Yehova anauza Aisiraeli kuti: “Kodi sindinakupulumutseni pamene Aiguputo,+ Aamori,+ Aamoni, Afilisiti,+ 12 Asidoni, Aamaleki ndi Amidiyani ankakuponderezani? Inu mutandilirira ndinakupulumutsani mʼmanja mwawo. 1 Samueli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
11 Koma Yehova anauza Aisiraeli kuti: “Kodi sindinakupulumutseni pamene Aiguputo,+ Aamori,+ Aamoni, Afilisiti,+ 12 Asidoni, Aamaleki ndi Amidiyani ankakuponderezani? Inu mutandilirira ndinakupulumutsani mʼmanja mwawo.