Salimo 68:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake. Salimo 113:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Chivumbulutso 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
4 Imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+ Imbirani Iye amene akudutsa mʼchipululu.* Dzina lake ndi Ya.*+ Sangalalani pamaso pake.