-
2 Mbiri 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ku Yerusalemu nakonso Yehosafati anaikako Alevi ena, ansembe ndi ena mwa atsogoleri a nyumba za makolo a Isiraeli, kuti akhale oweruza mʼmalo mwa Yehova ndipo aziweruza milandu ya anthu a ku Yerusalemu.+
-