-
1 Mbiri 29:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Choncho, Solomo anakhala pampando wachifumu wa Yehova+ monga mfumu mʼmalo mwa Davide bambo ake ndipo zinthu zinkamuyendera bwino. Aisiraeli onse ankamumvera.
-