Ezara 7:27, 28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yesaya 11:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku limenelo Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,* ku Hamati ndi mʼzilumba zamʼnyanja.+
11 Pa tsiku limenelo Yehova adzaperekanso dzanja lake kachiwiri kuti atenge anthu ake otsala kuchokera ku Asuri,+ ku Iguputo,+ ku Patirosi,+ ku Kusi,+ ku Elamu,+ ku Sinara,* ku Hamati ndi mʼzilumba zamʼnyanja.+