-
Yesaya 9:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mwapangitsa kuti mtundu ukhale waukulu.
Mwaupangitsa kuti usangalale kwambiri.
Iwo akusangalala pamaso panu
Ngati mmene anthu amasangalalira pa nthawi yokolola,
Ngati anthu amene amasangalala akamagawana katundu amene alanda.
-