Salimo 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ofatsa adzadya nʼkukhuta.+Anthu amene akufunafuna Yehova adzamutamanda.+ Musangalale ndi moyo* mpaka kalekale. Salimo 147:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Salimo 147:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye amabweretsa mtendere mʼdziko lako.+Ndipo amakupatsa tirigu wabwino* kwambiri.+
26 Ofatsa adzadya nʼkukhuta.+Anthu amene akufunafuna Yehova adzamutamanda.+ Musangalale ndi moyo* mpaka kalekale.