2 Samueli 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma mfumu inauza Zadoki kuti: “Tengani Likasa la Mulungu woona mubwerere nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandilola kuti ndibwerere mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+ Salimo 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”
25 Koma mfumu inauza Zadoki kuti: “Tengani Likasa la Mulungu woona mubwerere nalo mumzinda.+ Yehova akandikomera mtima adzandilola kuti ndibwerere mumzinda ndipo ndidzaliona. Ndidzaonanso malo amene limakhala.+
6 Iye adzawauza kuti: “Inetu ndasankha mfumu yanga+Ndipo ikulamulira ku Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”