- 
	                        
            
            Salimo 97:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
- 
                            - 
                                        9 Chifukwa inu Yehova, ndinu Wamʼmwambamwamba woyenera kulamulira dziko lonse lapansi. Ndinu wokwezeka kwambiri kuposa milungu ina yonse.+ 
 
-