-
Yesaya 13:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa iwo akuona,+
Katundu wamʼnyumba zawo adzalandidwa,
Ndipo akazi awo adzagwiriridwa.
-