-
Salimo 28:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,
Pamene ndikukweza manja anga, nditayangʼana kumene kuli chipinda chamkati chamʼmalo anu opatulika.+
-