-
Salimo 121:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Yehova adzakuteteza pa zochita zako zonse,*
Kuyambira panopa mpaka kalekale.
-
-
Miyambo 5:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,
Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+
-