-
Salimo 64:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ndibiseni ku ziwembu zachinsinsi za anthu oipa,+
Kwa gulu la anthu ochita zoipa.
-
-
Salimo 64:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Amafufuza njira zatsopano zochitira zinthu zoipa.
Mwachinsinsi amakonza njira zochitira ziwembu zawo mochenjera.+
Zimene munthu aliyense akuganiza mumtima mwake, nʼzovuta kuzimvetsa.
-