-
2 Samueli 22:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Iye amaphunzitsa manja anga kumenya nkhondo;
Manja anga angathe kukunga uta wakopa.*
-
-
Salimo 18:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Iye amaphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,
Manja anga angathe kukunga uta wakopa.*
-