Salimo 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anaweramitsa kumwamba pamene ankatsika,+Ndipo mdima wandiweyani unali pansi pa mapazi ake.+