2 Samueli 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Yehova+ kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka mʼmanja mwanga?” Yehova anauza Davide kuti: “Pita, Afilisitiwa ndiwapereka ndithu mʼmanja mwako.”+ Salimo 18:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake,+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.+
19 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Yehova+ kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwapereka mʼmanja mwanga?” Yehova anauza Davide kuti: “Pita, Afilisitiwa ndiwapereka ndithu mʼmanja mwako.”+
50 Iye amachita zazikulu kuti apulumutse mfumu yake,+Amasonyeza chikondi chokhulupirika kwa wodzozedwa wake,+Kwa Davide ndi mbadwa* zake mpaka kalekale.+