Yobu 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komatu zimenezi ndi kambali kakangʼono chabe ka zochita zake,+Ndipo tangomva kunongʼona kwapansipansi kwa mphamvu zake. Ndiye ndi ndani amene angamvetse mabingu ake amphamvu?”+ Salimo 139:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Aroma 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
14 Komatu zimenezi ndi kambali kakangʼono chabe ka zochita zake,+Ndipo tangomva kunongʼona kwapansipansi kwa mphamvu zake. Ndiye ndi ndani amene angamvetse mabingu ake amphamvu?”+