Salimo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wabwino komanso wolungama.+ Nʼchifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende mʼnjira yoyenera.+ Nahumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo pa nthawi yamavuto.+ Amadziwa* amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+ Mateyu 5:44, 45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Machitidwe 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
8 Yehova ndi wabwino komanso wolungama.+ Nʼchifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende mʼnjira yoyenera.+
7 Yehova ndi wabwino+ ndipo ndi malo achitetezo pa nthawi yamavuto.+ Amadziwa* amene amathawira kwa iye kuti apeze chitetezo.+