Deuteronomo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mwayamba kuonetsa mtumiki wanu ukulu wanu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene amachita ntchito zamphamvu ngati inu?+ 1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Chivumbulutso 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
24 ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, mwayamba kuonetsa mtumiki wanu ukulu wanu ndi dzanja lanu lamphamvu.+ Ndi mulungu winanso uti, kumwamba kapena padziko lapansi, amene amachita ntchito zamphamvu ngati inu?+