Salimo 117:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 117 Tamandani Yehova, inu mitundu yonse ya anthu.+Mulemekezeni, inu anthu a mitundu yonse.*+ Salimo 150:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chamoyo chilichonse chitamande Ya. Tamandani Ya!*+