-
Salimo 89:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Inu Yehova, kumwamba kudzakutamandani chifukwa cha ntchito zanu zodabwitsa,
Mpingo wa oyera anu udzakutamandani chifukwa ndinu wokhulupirika.
-