Yesaya 43:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zilombo zakutchire zidzandilemekeza,Komanso mimbulu ndi nthiwatiwa,Chifukwa ndimapereka madzi,Ndiponso mitsinje mʼchipululu,+Kuti anthu anga, wosankhidwa wanga,+ amwe,
20 Zilombo zakutchire zidzandilemekeza,Komanso mimbulu ndi nthiwatiwa,Chifukwa ndimapereka madzi,Ndiponso mitsinje mʼchipululu,+Kuti anthu anga, wosankhidwa wanga,+ amwe,