-
Oweruza 11:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Kenako Yefita anabwerera kwawo ku Mizipa+ ndipo akufika anangoona mwana wake wamkazi akubwera kudzamʼchingamira, akuimba maseche komanso akuvina. Iye anali mwana yekhayo amene anali naye. Analibenso mwana wina wamwamuna kapena wamkazi.
-