-
Salimo 49:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Pakamwa panga padzalankhula zinthu zanzeru,
Ndipo zimene ndikuganizira mozama mumtima mwanga+ zidzasonyeza kuti ndine wozindikira.
-
-
Salimo 51:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Inu Yehova, tsegulani milomo yangayi,
Kuti pakamwa panga patamande inu.+
-