-
Salimo 63:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Koma mfumu idzasangalala ndi zimene Mulungu adzaichitire.
Munthu aliyense wolumbira mʼdzina la Mulungu adzasangalala kwambiri,*
Chifukwa pakamwa pa anthu olankhula zabodza padzatsekedwa.
-